Levitiko 13:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Pamenepo azitentha chovalacho, nsalu ya ubweya wa nkhosa kapena nsalu ina iliyonse,+ kapena zilizonse zopangidwa ndi chikopa, zimene zagwidwa ndi nthenda ya khateyo, chifukwa khate limenelo ndi loopsa.+ Zizitenthedwa pamoto.
52 Pamenepo azitentha chovalacho, nsalu ya ubweya wa nkhosa kapena nsalu ina iliyonse,+ kapena zilizonse zopangidwa ndi chikopa, zimene zagwidwa ndi nthenda ya khateyo, chifukwa khate limenelo ndi loopsa.+ Zizitenthedwa pamoto.