Levitiko 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku la 7 azimeta tsitsi lake lonse lakumutu,+ ndevu zake zonse ndi nsidze zonse. Azimeta tsitsi lake lonse, ndipo azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje. Akatero, azikhala woyera.
9 Pa tsiku la 7 azimeta tsitsi lake lonse lakumutu,+ ndevu zake zonse ndi nsidze zonse. Azimeta tsitsi lake lonse, ndipo azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje. Akatero, azikhala woyera.