17 Koma mafuta amene atsala pachikhatho cha wansembe aziwapaka m’munsi pakhutu la kudzanja lamanja la munthu amene akudziyeretsayo, pachala chake chamanthu kudzanja lamanja, ndi pachala chake chachikulu chakumwendo wa kudzanja lamanja pamene anam’paka magazi a nsembe ya kupalamula.+