Levitiko 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno wansembe azipereka nsembe yopsereza ndi nsembe yambewu+ paguwa lansembe. Akatero, wansembe+ azim’phimbira machimo,+ ndipo munthuyo azikhala woyera.+
20 Ndiyeno wansembe azipereka nsembe yopsereza ndi nsembe yambewu+ paguwa lansembe. Akatero, wansembe+ azim’phimbira machimo,+ ndipo munthuyo azikhala woyera.+