-
Levitiko 14:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiyeno wansembe azipha nkhosa yaing’ono yamphongo ya nsembe ya kupalamula. Akatero azitenga ena mwa magazi a nsembe ya kupalamulayo n’kuwapaka m’munsi pakhutu la kudzanja lamanja la munthu amene akudziyeretsayo, pachala chake chamanthu kudzanja lamanja, ndi pachala chake chachikulu chakumwendo wa kudzanja lamanja.+
-