Levitiko 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo wansembeyo azithira ena mwa mafutawo pachikhatho cha dzanja lake lamanzere.+