Levitiko 14:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 wansembe azilamula kuti achotse+ miyala imene ili ndi nthendayo, ndi kuti akaiponye kunja kwa mzinda, kumalo odetsedwa.
40 wansembe azilamula kuti achotse+ miyala imene ili ndi nthendayo, ndi kuti akaiponye kunja kwa mzinda, kumalo odetsedwa.