Levitiko 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwamuna akagonana ndi mkazi ameneyu, azikhala wodetsedwa chifukwa chakuti mkaziyo akusamba.+ Zikatero, mwamunayo azikhala wodetsedwa masiku 7, ndipo bedi lililonse limene angagonepo lizikhala lodetsedwa. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:24 Nsanja ya Olonda,6/1/1989, tsa. 14
24 Mwamuna akagonana ndi mkazi ameneyu, azikhala wodetsedwa chifukwa chakuti mkaziyo akusamba.+ Zikatero, mwamunayo azikhala wodetsedwa masiku 7, ndipo bedi lililonse limene angagonepo lizikhala lodetsedwa.