-
Levitiko 15:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 “‘Mkazi akakha magazi kwa masiku ambiri+ pamene si nthawi yake yokhala wodetsedwa chifukwa cha kusamba,+ kapena akapitiriza kukha magazi nthawi yake yokhala wodetsedwa chifukwa cha kusamba kwake itatha, masiku onse pamene iye akukha magaziwo azikhala ngati mmene amakhalira pa nthawi yake yokhala wodetsedwa chifukwa cha kusamba. Iye ndi wodetsedwa.
-