Levitiko 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aliyense wokhudza+ zinthuzo azikhala wodetsedwa, ndipo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.
27 Aliyense wokhudza+ zinthuzo azikhala wodetsedwa, ndipo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.