Levitiko 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda, ndi kubwera nawo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+
29 Ndiyeno pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda, ndi kubwera nawo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+