Levitiko 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Lamulo limeneli ndi lokhudzanso mkazi wodetsedwa chifukwa cha kusamba+ kwake, ndi aliyense amene ali ndi nthenda yakukha kumaliseche,+ kaya mwamuna kapena mkazi ndiponso mwamuna wogonana ndi mkazi wodetsedwa.’”
33 Lamulo limeneli ndi lokhudzanso mkazi wodetsedwa chifukwa cha kusamba+ kwake, ndi aliyense amene ali ndi nthenda yakukha kumaliseche,+ kaya mwamuna kapena mkazi ndiponso mwamuna wogonana ndi mkazi wodetsedwa.’”