Levitiko 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose pambuyo pa imfa ya ana awiri a Aroni, amene anafa+ chifukwa choonekera pamaso pa Yehova mosavomerezeka.
16 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose pambuyo pa imfa ya ana awiri a Aroni, amene anafa+ chifukwa choonekera pamaso pa Yehova mosavomerezeka.