Levitiko 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azivala mkanjo wopatulika wowomba,+ kabudula wansalu+ wobisa thupi lake, lamba wansalu wa pamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+
4 Azivala mkanjo wopatulika wowomba,+ kabudula wansalu+ wobisa thupi lake, lamba wansalu wa pamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+