Levitiko 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongoyo,+ ndi kuwadontheza ndi chala chake patsogolo pa chivundikiro, chakum’mawa. Azidontheza+ magaziwo ndi chala chake maulendo 7 patsogolo pa chivundikirocho.+
14 “Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongoyo,+ ndi kuwadontheza ndi chala chake patsogolo pa chivundikiro, chakum’mawa. Azidontheza+ magaziwo ndi chala chake maulendo 7 patsogolo pa chivundikirocho.+