Levitiko 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Akatero azituluka ndi kupita kuguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova kuti akaliphimbire machimo. Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongo ndi a mbuzi n’kuwapaka panyanga zonse za guwa lansembe.+
18 “Akatero azituluka ndi kupita kuguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova kuti akaliphimbire machimo. Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongo ndi a mbuzi n’kuwapaka panyanga zonse za guwa lansembe.+