Levitiko 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Akamaliza kuphimbira machimo+ malo oyera, chihema chokumanako ndi guwa lansembe, azibweretsanso mbuzi yamoyo ija.+
20 “Akamaliza kuphimbira machimo+ malo oyera, chihema chokumanako ndi guwa lansembe, azibweretsanso mbuzi yamoyo ija.+