Levitiko 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Pamenepo Aroni azilowa m’chihema chokumanako ndi kuvula zovala zake zimene anavala polowa m’malo oyera, n’kuzisiya momwemo.+
23 “Pamenepo Aroni azilowa m’chihema chokumanako ndi kuvula zovala zake zimene anavala polowa m’malo oyera, n’kuzisiya momwemo.+