Levitiko 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Akatero azisamba thupi lonse+ m’malo oyera+ ndi kuvala zovala zake.+ Kenako azituluka kukapereka nsembe yake yopsereza+ ndi nsembe yopsereza ya anthuwo+ ndipo aziphimba machimo ake ndi a anthuwo.+
24 Akatero azisamba thupi lonse+ m’malo oyera+ ndi kuvala zovala zake.+ Kenako azituluka kukapereka nsembe yake yopsereza+ ndi nsembe yopsereza ya anthuwo+ ndipo aziphimba machimo ake ndi a anthuwo.+