Levitiko 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Munthu+ amene anapititsa mbuzi ya Azazeli uja+ azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse.+ Akatero angathe kulowa mumsasa.
26 “Munthu+ amene anapititsa mbuzi ya Azazeli uja+ azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse.+ Akatero angathe kulowa mumsasa.