Levitiko 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati sanachape zovala zakezo komanso sanasambe thupi lonse, ameneyo ayenera kuyankha mlandu wa cholakwa chake.’”+
16 Koma ngati sanachape zovala zakezo komanso sanasambe thupi lonse, ameneyo ayenera kuyankha mlandu wa cholakwa chake.’”+