Levitiko 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Motero inu muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu,+ musachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi.
26 Motero inu muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu,+ musachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi.