Levitiko 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 M’chaka chachisanu, muzidya zipatso zake ndipo mtengowo udzakuberekerani zipatso zochuluka.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, ptsa. 6-7
25 M’chaka chachisanu, muzidya zipatso zake ndipo mtengowo udzakuberekerani zipatso zochuluka.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.