-
Levitiko 23:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kwa masiku 7, muzipereka kwa Yehova nsembe zotentha ndi moto. Pa tsiku la 7 muzichita msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yolemetsa.’”
-