Levitiko 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Kuchokera pa tsiku lotsatana ndi sabata, pamene munabweretsa mtolo kuti ukhale nsembe yoweyula,* muziwerenga masabata* 7,+ ndipo akwane ndendende.
15 “‘Kuchokera pa tsiku lotsatana ndi sabata, pamene munabweretsa mtolo kuti ukhale nsembe yoweyula,* muziwerenga masabata* 7,+ ndipo akwane ndendende.