Levitiko 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi+ monga nsembe yamachimo, ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yachiyanjano.+
19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi+ monga nsembe yamachimo, ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yachiyanjano.+