Levitiko 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pagulu lililonse la mikateyo uike lubani weniweni. Lubaniyo aziperekedwa nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova monga chikumbutso+ choimira mkate.
7 Pagulu lililonse la mikateyo uike lubani weniweni. Lubaniyo aziperekedwa nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova monga chikumbutso+ choimira mkate.