-
Levitiko 25:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 “‘Mlendo wokhala pakati panu akalemera, ndipo m’bale wanu amene akukhala naye pafupi wasauka, moti wakadzigulitsa kwa mlendoyo, kapena kwa wina wa m’banja la mlendoyo,
-