Levitiko 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati msinkhu wa munthuyo ndi wapakati pa mwezi umodzi ndi zaka zisanu, akakhala wamwamuna mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva asanu,+ ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli asiliva atatu.
6 Ngati msinkhu wa munthuyo ndi wapakati pa mwezi umodzi ndi zaka zisanu, akakhala wamwamuna mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva asanu,+ ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli asiliva atatu.