Levitiko 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ngati chopereka chake ndi nyama yodetsedwa+ imene anthu sangaipereke nsembe kwa Yehova,+ azikaonetsa nyamayo kwa wansembe.+
11 Koma ngati chopereka chake ndi nyama yodetsedwa+ imene anthu sangaipereke nsembe kwa Yehova,+ azikaonetsa nyamayo kwa wansembe.+