Levitiko 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo wansembe azinena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo wa nyamayo+ umene wansembe wanena uzikhala womwewo.
12 Ndipo wansembe azinena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo wa nyamayo+ umene wansembe wanena uzikhala womwewo.