Levitiko 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ngati wopereka mundayo angauwombole, azipereka mtengo wake woikidwiratu ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu, akatero mundawo uzikhaladi wake.+
19 Koma ngati wopereka mundayo angauwombole, azipereka mtengo wake woikidwiratu ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu, akatero mundawo uzikhaladi wake.+