Numeri 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mbadwa za Dani,+ anazilemba mayina malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.
38 Mbadwa za Dani,+ anazilemba mayina malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.