Numeri 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Chigawo cha mafuko atatu cha Dani ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumpoto. Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.
25 “Chigawo cha mafuko atatu cha Dani ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumpoto. Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.