Numeri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Nsanja ya Olonda,4/15/1992, tsa. 12
9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+