Numeri 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 nsalu za mpanda+ wa bwalo, nsalu yotchinga+ pakhomo la bwalo lozungulira chihema chopatulika, ndi guwa lansembe, ndiponso zingwe za chinsalu chake,+ komanso ntchito zonse zokhudza utumikiwu.
26 nsalu za mpanda+ wa bwalo, nsalu yotchinga+ pakhomo la bwalo lozungulira chihema chopatulika, ndi guwa lansembe, ndiponso zingwe za chinsalu chake,+ komanso ntchito zonse zokhudza utumikiwu.