Numeri 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Amuna onse owerengedwa, kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo, analipo 8,600. Ntchito ya amenewa inali kutumikira pamalo oyera.+
28 Amuna onse owerengedwa, kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo, analipo 8,600. Ntchito ya amenewa inali kutumikira pamalo oyera.+