Numeri 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mabanja a ana a Kohati anali kumanga msasa wawo kum’mwera kwa chihema chopatulika.+