Numeri 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Merari anali Zuriyeli, mwana wa Abihaili. Iwo anali kumanga msasa wawo kumpoto kwa chihema chopatulika.+
35 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Merari anali Zuriyeli, mwana wa Abihaili. Iwo anali kumanga msasa wawo kumpoto kwa chihema chopatulika.+