Numeri 3:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo anali kusamaliranso nsanamira+ za mpanda wozungulira bwalo ndiponso zitsulo zokhazikapo nsanamirazo,+ komanso zikhomo ndi zingwe zake zolimbitsira nsanamirazo.
37 Iwo anali kusamaliranso nsanamira+ za mpanda wozungulira bwalo ndiponso zitsulo zokhazikapo nsanamirazo,+ komanso zikhomo ndi zingwe zake zolimbitsira nsanamirazo.