Numeri 3:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kenako Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Uwerenge ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli, kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo,+ ndipo ulembe mayina awo.
40 Kenako Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Uwerenge ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli, kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo,+ ndipo ulembe mayina awo.