Numeri 3:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli.+ Unditengerenso ziweto zonse za Alevi m’malo mwa ziweto zonse zoyamba kubadwa za ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova.” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:41 Nsanja ya Olonda,7/1/1995, tsa. 16
41 Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli.+ Unditengerenso ziweto zonse za Alevi m’malo mwa ziweto zonse zoyamba kubadwa za ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova.”