Numeri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu n’kuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira zake zozimitsira nyale,+ zoikamo phulusa la zingwe za nyale,+ ndi ziwiya zake zonse+ zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.
9 Ndiyeno azitenga nsalu yabuluu n’kuphimbira choikapo nyale,+ pamodzi ndi nyale zake,+ zopanira zake zozimitsira nyale,+ zoikamo phulusa la zingwe za nyale,+ ndi ziwiya zake zonse+ zosungiramo mafuta ogwiritsa ntchito nthawi zonse.