-
Numeri 4:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Azinyamulanso nsalu za mpanda+ wa bwalo ndi nsalu yotchinga+ khomo la mpanda umene umazungulira chihema chopatulika ndi guwa lansembe. Ndiponso azinyamula zingwe zolimbitsira mpandawo, ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wawo, pamodzi ndi zinthu zina zonse zogwirira ntchito zawo za nthawi zonse. Umenewu ndiwo utumiki wawo.
-