-
Numeri 5:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Wansembeyo azitenga madzi opatulika m’chiwiya chadothi. Azitengakonso fumbi lapansi m’chihema chopatulika, n’kulithira m’madziwo.
-