Numeri 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ngati munthu wina wafera pambali pake mwadzidzidzi,+ moti Mnaziriyo waipitsa mutu umene uli ndi chizindikiro cha unaziri wake pokhudza mtembowo, amete tsitsi+ la kumutu kwake pa tsiku la kuyeretsedwa kwake. Alimete pa tsiku la 7.
9 Koma ngati munthu wina wafera pambali pake mwadzidzidzi,+ moti Mnaziriyo waipitsa mutu umene uli ndi chizindikiro cha unaziri wake pokhudza mtembowo, amete tsitsi+ la kumutu kwake pa tsiku la kuyeretsedwa kwake. Alimete pa tsiku la 7.