Numeri 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthuyo ayambirenso masiku ake odzipereka kwa Yehova ngati Mnaziri,+ ndipo abweretse nkhosa yaing’ono yamphongo yosapitirira chaka chimodzi monga nsembe ya kupalamula.+ Masiku oyamba aja sadzawerengedwa chifukwa anaipitsa unaziri wake.
12 Munthuyo ayambirenso masiku ake odzipereka kwa Yehova ngati Mnaziri,+ ndipo abweretse nkhosa yaing’ono yamphongo yosapitirira chaka chimodzi monga nsembe ya kupalamula.+ Masiku oyamba aja sadzawerengedwa chifukwa anaipitsa unaziri wake.