Numeri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano atsogoleriwo anafika ndi zopereka zawo pamwambo wotsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku lodzoza guwalo. Anabweretsa zopereka zawozo kuguwa lansembe.
10 Tsopano atsogoleriwo anafika ndi zopereka zawo pamwambo wotsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku lodzoza guwalo. Anabweretsa zopereka zawozo kuguwa lansembe.