Numeri 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kaperekedwe ka zopereka zotsegulira guwalo kakhale kotere, pa tsiku limodzi mtsogoleri mmodzi azipereka zopereka zake.”+
11 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kaperekedwe ka zopereka zotsegulira guwalo kakhale kotere, pa tsiku limodzi mtsogoleri mmodzi azipereka zopereka zake.”+