Numeri 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa tsiku la 7 panali mtsogoleri wa ana a Efuraimu, Elisama+ mwana wa Amihudi.